Salvation Devotions

Kupulumutsa Ena Pogwiritsa Ntchito Chuma Kapena Zomwe Mulungu Watidalitsa Nazo.

Mabuku: Salimo 1:1-6, Habakuku 1:1-17, Mateyu 14:13-21

Mawu Oyamba

Mulungu akupereka njira zosiyanasiyana kwa aliyense kuti afikire ena kuti enawonso apulumutsidwe. Mwachitsanzo, dzulo Abusa a Masambuka anafotokoza kuti anthu amene anamanga Kachisi wathu wa Zomba CCAP onse anamwalira kalekale koma anagwiritsa nzeru, luso, mphamvu ndi chuma chawo kuti anthu ambiri kuphatikiza...

Read more

 

Phukusi La Chipulumutso

Mawu Oyamba

M’kati mwa phukusi mumakhala zinthu ndipo umayenera kulimasula kuti uone ndi kupeza zomwe zili m’kaimo. Mu chipulumutso muli zinthu zimene zikuyamba m’moyo uno pansi pano mpaka tsiku lopita kumwamba. Pali zinthu zimene tikuyenra kuchitika ngakhale pansi panopa kuti tikapeze phindu la chipulumutso.

Kutambasula Mawu

Read more

 

Enjoying The Greatness Of Your Salvation

Bible Readings: Isaiah 43:1-7 1 Peter 1: 10-12, John 1: 12

Introduction

Salvation is central to the church of God. We cannot exhaust talking about it.
Two points of focus:

  1. We are saved by grace
  2. This grace is great

Story of salvation. We are saved by grace through the love ...

Read more

 


About Us

Zomba CCAP congregation, located in Zomba City, the old capital of Malawi, was established in 1898, and currently boasts 1,638 Christians, of which 115 are church elders and 103 church deacons. It has vibrant women and youth ministries, and a management team that co-ordinates the work of eleven committees, among which are the partnership, evangelism and intercessory, and music committee, as well as faith and works committee... Read more

Announcements & Events

Explosion 2023 Posted: 13 Apr, 2023
Zomba CCAP Holy Week Time Table Posted: 3 Apr, 2023

Address

Zomba C.C.A.P.
Chimbiya Road
P.O. Box 355, Zomba
+265 995 089 475

Newsletter