Koma Si Monga Mwakufuna Kwanga Koma Chifuniro Chanu Ndithu
Mawu Owerengedwa: Yesaya 53:1-7, Ahebri 10:32-36, Mateyu 26:36-50
Mawu Oyamba
“Ambuye ngati mufuna chikho ichi chindipitirire. Koma si monga mwakufuna kwanga koma chifuniro chanu ndithu.” Yesaya 53
akufotokoza molunjika za kubwera kwa Ambuye Yesu ndi za mazunzo ake. Zimenezi sizinangochitika ayi, zinali zitanenedwa kale ku chipangano chakal...