Sermons

A Church With Jesus Christ: The Only Hope For This Generation

Bible Readings: Isaiah 60:1-5, Colossians 1:24-29, Psalms 82:1-8

Introduction

First of all let me ask you a question, ever since we received Jesus, Have we become the answer to the Generation?

In Isaiah 60, the bible is explaining the message of hope that was given to the Israelites, showing them that of their glory. The bible stress up t...

Read more

 

Lamulo Lachisanu Ndi Chinayi (9): Usamnamizire Mnzako

Eksodo 20:16

Mawu Otsogolera

Lero tipitiriza kukambirana za Malamulo khumi monga takhalatikuchitira m’miyezi iwiri yapitayi. Lerotikambirana pa za lamulo lachisanu ndi chinayi. Koma tisanayang’ane lamuloli tiyeni tione mfundo izi za malamulo khumi onse.

  1. Malamulo khumi anali mawu amene anachita kuchokera kwa mwini Mulungu. Sakuyener...

    Read more

     

Lamulo Lachisanu Ndi Chitatu (8): Usabe

Mawu Otsogolera

Mulungu anapanga malamulo kuti munthu ndi zolengedwa zina zonse zipindule. Chinthu chilichonse chomwe Mulungu anachilenga chimachitika ndi chikonzero cha Mulungu mwini ndipo pakakhala kusemphana ndi chikonzerochi zinthuzo zimaonongeka. Mwachitsanzo, nsomba zinalengedwa kuti zizikhala m’madzi. Ndi chifukwa chake zikakhala pamtunda zimafa. Dzuwa limatulikira kum’mawa ndi kukolowera kum...

Read more

 

About Us

Zomba CCAP congregation, located in Zomba City, the old capital of Malawi, was established in 1898, and currently boasts 1,638 Christians, of which 115 are church elders and 103 church deacons. It has vibrant women and youth ministries, and a management team that co-ordinates the work of eleven committees, among which are the partnership, evangelism and intercessory, and music committee, as well as faith and works committee... Read more

Announcements & Events

Explosion 2023 Posted: 13 Apr, 2023
Zomba CCAP Holy Week Time Table Posted: 3 Apr, 2023

Address

Zomba C.C.A.P.
Chimbiya Road
P.O. Box 355, Zomba
+265 995 089 475

Newsletter