Scriptures Devotions

Koma Si Monga Mwakufuna Kwanga Koma Chifuniro Chanu Ndithu

Mawu Owerengedwa: Yesaya 53:1-7, Ahebri 10:32-36, Mateyu 26:36-50

Mawu Oyamba

“Ambuye ngati mufuna chikho ichi chindipitirire. Koma si monga mwakufuna kwanga koma chifuniro chanu ndithu.” Yesaya 53
akufotokoza molunjika za kubwera kwa Ambuye Yesu ndi za mazunzo ake. Zimenezi sizinangochitika ayi, zinali zitanenedwa kale ku chipangano chakal...

Read more

 

Kumvetsetsa Tanthauzo La Imfa Ndi Kuuka Kwa Ambuye Wathu Yesu Khristu

Mabuku Genesis 3:19 Akolose 1:23, Akolose 2:16

Mawu Oyamba

Genesis ndi buku lolembedwa ndi Mose ndipo limatchedwa kuti bukhu lachiyambi (chilengedwe) cha munthu, chiyambi cha tchimo ndi chipulumutso. Lero chiyambi cha tchimo ndi chipulumutso cha munthu. Bukuli limatidziwitsa za Mulungu ndi mphamvu yake. Atalenga zonse anakhazikitsa ubale wapadera ndi munthu. Mulungu anapatsa munthu ulamuliro pa zinthu z...

Read more

 


About Us

Zomba CCAP congregation, located in Zomba City, the old capital of Malawi, was established in 1898, and currently boasts 1,638 Christians, of which 115 are church elders and 103 church deacons. It has vibrant women and youth ministries, and a management team that co-ordinates the work of eleven committees, among which are the partnership, evangelism and intercessory, and music committee, as well as faith and works committee... Read more

Announcements & Events

Explosion 2023 Posted: 13 Apr, 2023
Zomba CCAP Holy Week Time Table Posted: 3 Apr, 2023

Address

Zomba C.C.A.P.
Chimbiya Road
P.O. Box 355, Zomba
+265 995 089 475

Newsletter